Ma subtitles amapezeka podina batani la CC. Tsitsani
Malo osungila mafilimu ndi nyimbo za Chiyao m’thumba mwanu!
Mafilimuwa ndi aulere kuti muwone, kukopera, kugawa, ndi kukambirana.


Mafilimu Okondedwa
Nawa mafilimu omwe amakondedwa, mupeza ambiri pa Yao Story App.


Kodi mungatani mutakumana ndi munthu amene anakuberani? Kodi mungamukhululukire? Kodi wakuba ingasinthe?


Munthu wina wolemera wabizinesi amaika ndalama zake kwa achibale ake atatu. Kodi adzaika ndalamazo mwanzeru kapena adzapezeka opusa akabwerera kunyumba mosayembekezereka?


Kodi mumathawira kuti tsiku limene zithu sizikuyenda bwino? Ndani angakuthandizeni banja lanu likakukanani?


Mtsikana akubwerera kunyumba ndi mwana wamng’ono mwamanyazi.Kodi chikhululuko cha atate ake chizatha kuyanjanisanso banja lawo pamodzi.

